Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 140:2 - Buku Lopatulika

2 amene adzipanga zoipa mumtima mwao; masiku onse amemeza nkhondo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 amene adzipanga zoipa mumtima mwao; masiku onse amemeza nkhondo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Iwo amalingalira mumtima mwao kuti achite zoipa, amautsa nkhondo nthaŵi zonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 amene mu mtima mwawo amakonza zinthu zoyipa ndi kuyambitsa nkhondo tsiku lililonse.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 140:2
16 Mawu Ofanana  

Ine ndikuti, Mtendere; koma polankhula ine, iwowa akuti, Nkhondo.


Pakuti anakupangirani choipa, anapangana chiwembu, osakhoza kuchichita.


Alingirira zopanda pake pakama pake; adziika panjira posati pabwino; choipa saipidwa nacho.


Ndipo anditchera misampha iwo akufuna moyo wanga; ndipo iwo akuyesa kundichitira choipa alankhula zoononga, nalingirira zonyenga tsiku lonse.


Amemezana, alalira, atchereza mapazi anga, popeza alindira moyo wanga.


Pakuti onani, alalira moyo wanga; amphamvu andipangira chiwembu, osachimwa, osalakwa ine, Yehova,


Mudzamvumvulukira munthu mpaka liti, kumupha iye, nonsenu, monga khoma lopendekeka, ndi mpanda woweyeseka?


Chinyengo chili m'mitima ya oganizira zoipa; koma aphungu a mtendere amakondwa.


Pakuti asendera nao mtima wao wakunga ng'anjo ya mkate, pokhala alikulalira; wootcha mkate wao agona usiku wonse, m'mawa iyaka ngati moto wa malawi.


Mwa iwe watuluka wina wolingalira choipa chotsutsana ndi Yehova, ndiye phungu wopanda pake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa