Masalimo 140:1 - Buku Lopatulika1 Ndilanditseni, Yehova, kwa munthu woipa; ndisungeni kwa munthu wachiwawa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndilanditseni, Yehova, kwa munthu woipa; ndisungeni kwa munthu wachiwawa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pulumutseni, Inu Chauta, kwa anthu oipa. Tchinjirizeni kwa anthu ankhanza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Landitseni Yehova kwa anthu oyipa; tetezeni kwa anthu ankhanza, Onani mutuwo |