Masalimo 139:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo mupenye ngati ndili nao mayendedwe oipa, nimunditsogolere panjira yosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo mupenye ngati ndili nao mayendedwe oipa, nimunditsogolere pa njira yosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Muwone ngati ndimatsata njira yoipa iliyonse, ndipo munditsogolere m'njira yanu yamuyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Onani ngati muli mayendedwe aliwonse oyipa mwa ine, ndipo munditsogolere mʼnjira yanu yamuyaya. Onani mutuwo |