Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 14:7 - Buku Lopatulika

7 Mwenzi chipulumutso cha Israele chitachokera ku Ziyoni! Pakubweretsa Yehova anthu ake a m'nsinga, pamenepo adzakondwera Yakobo, nadzasekera Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Mwenzi chipulumutso cha Israele chitachokera ku Ziyoni! Pakubweretsa Yehova anthu ake a m'nsinga, pamenepo adzakondwera Yakobo, nadzasekera Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Chibwere ndithu chipulumutso cha Israele kuchokera ku Ziyoni. Chauta akadzaŵabwezera ufulu anthu ake, Yakobe adzakondwera, Israele adzasangalala kwambiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ndithu, chipulumutso cha Israeli chidzachokera ku Ziyoni! Pamene Yehova abwezeretsa ufulu wa anthu ake, Yakobo akondwere ndipo Israeli asangalale!

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 14:7
4 Mawu Ofanana  

Pobweza Yehova ukapolo wa Ziyoni, tinakhala ngati anthu akulota.


Ha, chipulumutso cha Israele chichokere mu Ziyoni! Pakubweretsa Mulungu anthu ake a m'ndende, Yakobo adzakondwera, Israele adzasekera.


Munachita zovomereza dziko lanu, Yehova; munabweza ukapolo wa Yakobo.


ndipo oomboledwa a Yehova adzabwera, nadzafika ku Ziyoni alikuimba; kukondwa kosatha kudzakhala pa mitu yao; iwo adzakhala ndi kusekerera ndi kukondwa, ndipo chisoni ndi kuusa moyo kudzachoka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa