Masalimo 14:6 - Buku Lopatulika6 Munyazitsa uphungu wa wozunzika, koma Yehova ndiye pothawira pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Munyazitsa uphungu wa wozunzika, koma Yehova ndiye pothawira pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Inu anthu oipa, mumayesa kusokoneza zolinga za anthu osauka, koma iwo amathaŵira kwa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Inu ochita zoyipa mumalepheretsa chikonzero cha anthu osauka, koma Yehova ndiye pothawirapo pawo. Onani mutuwo |
Mukavomereza tsono, pakumva mau a lipenga, chitoliro, zeze, sansi, chisakasa, ndi ngoli, ndi zoimbitsa zilizonse, kugwadira ndi kulambira fano ndinalipanga, chabwino; koma mukapanda kulambira, mudzaponyedwa nthawi yomweyi m'kati mwa ng'anjo yotentha yamoto; ndipo mulungu yemwe adzakulanditsani m'manja mwanga ndani?