Masalimo 14:4 - Buku Lopatulika4 Kodi onse ochita zopanda pake sadziwa kanthu? Pakudya anthu anga monga akudya mkate, ndipo saitana pa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Kodi onse ochita zopanda pake sadziwa kanthu? Pakudya anthu anga monga akudya mkate, ndipo saitana pa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Kani anthu oipaŵa alibe nzeru chotere? Iwo amameza anthu anga, kuŵayesa chakudya, ndipo samutama Chauta mopemba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kodi anthu ochita zoyipawa sadziwa chilichonse? Akudya anthu anga ngati chakudya chawo ndipo satamanda Yehova? Onani mutuwo |