Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 136:9 - Buku Lopatulika

9 Mwezi ndi nyenyezi ziweruze usiku; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Mwezi ndi nyenyezi ziweruze usiku; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Mwezi ndi nyenyezi kuti zizilamulira usiku, pakuti chikondi chake nchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Mwezi ndi nyenyezi zilamulire usiku, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 136:9
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Mulungu anapanga zounikira zazikulu ziwiri; chounikira chachikulu chakulamulira usana, chounikira chaching'ono chakulamulira usiku, ndi nyenyezi zomwe.


ngati ndalambira dzuwa lilikuwala, kapena mwezi ulikuyenda monyezimira;


Usana ndi wanu, usikunso ndi wanu, munakonza kuunika ndi dzuwa.


Pakuona ine thambo la kumwamba lanu, ntchito ya zala zanu, mwezi ndi nyenyezi, zimene munazikhazika,


munthu ndani kuti mumkumbukira? Ndi mwana wa munthu kuti mucheza naye?


Yehova atero, amene apatsa dzuwa kuti liunikire usana, ndi malemba a mwezi ndi a nyenyezi kuti aunikire usiku, amene atonthoza nyanja, pamene mafunde ake agavira; Yehova wa makamu ndi dzina lake:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa