Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 136:8 - Buku Lopatulika

8 Dzuwa liweruze usana; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Dzuwa liweruze usana; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Dzuŵa kuti lizilamulira usana, pakuti chikondi chake nchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Dzuwa lilamulire usana, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 136:8
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Mulungu anapanga zounikira zazikulu ziwiri; chounikira chachikulu chakulamulira usana, chounikira chaching'ono chakulamulira usiku, ndi nyenyezi zomwe.


Mlemekezeni, dzuwa ndi mwezi; mlemekezeni, nyenyezi zonse zounikira.


Usana ndi wanu, usikunso ndi wanu, munakonza kuunika ndi dzuwa.


Yehova atero, amene apatsa dzuwa kuti liunikire usana, ndi malemba a mwezi ndi a nyenyezi kuti aunikire usiku, amene atonthoza nyanja, pamene mafunde ake agavira; Yehova wa makamu ndi dzina lake:


kotero kuti mukakhale ana a Atate wanu wa Kumwamba; chifukwa Iye amakwezera dzuwa lake pa oipa ndi pa abwino, namavumbitsira mvula pa olungama ndi pa osalungama.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa