Masalimo 136:7 - Buku Lopatulika7 Amene analenga miuni yaikulu; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Amene analenga miuni yaikulu; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Adalenga miyuni yaikulu yamumlengalenga, pakuti chikondi chake nchamuyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Amene anapanga miyuni ikuluikulu, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. Onani mutuwo |