Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 136:23 - Buku Lopatulika

23 Amene anatikumbukira popepuka ife; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Amene anatikumbukira popepuka ife; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Adatikumbukira pamene adani adatigonjetsa, pakuti chikondi chake nchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Amene anatikumbukira ife anthu opeputsidwa, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 136:23
13 Mawu Ofanana  

Ndipo Mulungu anakumbukira Nowa ndi zamoyo zonse, ndi nyama zonse zimene zinali pamodzi naye m'chingalawamo; ndipo Mulungu anapititsa mphepo padziko lapansi, naphwa madzi;


anasamalira pemphero la iwo akusowa konse, osapepula pemphero lao.


Amene autsa wosauka kumchotsa kufumbi, nakweza waumphawi kumchotsa kudzala.


Yehova asunga opusa; ndidafooka ine, koma anandipulumutsa.


Tamverani kufuula kwanga; popeza ndisauka kwambiri; ndilanditseni kwa iwo akundilondola; popeza andipambana.


M'mazunzo ao onse Iye anazunzidwa, ndipo mthenga wakuimirira pamaso pake anawapulumutsa; m'kukonda kwake ndi m'chisoni chake Iye anawaombola, nawabereka nawanyamula masiku onse akale.


chifukwa Iye anayang'anira umphawi wa mdzakazi wake; pakuti taonani, kuyambira tsopano, anthu a mibadwo yonse adzanditchula ine wodala.


Iye anatsitsa mafumu pa mipando yao yachifumu, ndipo anakweza aumphawi.


Popeza Yehova adzaweruza anthu ake, nadzachitira nsoni anthu ake; pakuona Iye kuti mphamvu yao yatha, wosatsala womangika kapena waufulu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa