Masalimo 136:22 - Buku Lopatulika22 Cholowa cha kwa Israele mtumiki wake; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Chosiyira cha kwa Israele mtumiki wake; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Choloŵa cha Israele mtumiki wake, pakuti chikondi chake nchamuyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Cholowa cha mtumiki wake Israeli; pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. Onani mutuwo |