Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 136:21 - Buku Lopatulika

21 Ndipo anapereka dziko lao likhale cholowa; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Ndipo anapereka dziko lao likhale chosiyira; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Napereka dziko la mafumuwo kuti likhale choloŵa, pakuti chikondi chake nchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Napereka dziko lawo ngati cholowa, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 136:21
11 Mawu Ofanana  

Ndipo anawapatsa maiko a amitundu; iwo ndipo analanda zipatso za ntchito ya anthu:


Ndipo anapereka dziko lao likhale cholowa, cholowa cha kwa Israele anthu ake.


Ndipo anapirikitsa amitundu pamaso pao, nawagawira cholowa chao, ndi muyeso, nakhalitsa mafuko a Israele m'mahema mwao.


Koma iwe, Israele, mtumiki wanga, Yakobo, amene ndinakusankha, mbeu ya Abrahamu bwenzi langa;


Ndipo ndinauza inu muja, ndi kuti, Yehova Mulungu wanu wakupatsani dziko ili likhale lanulanu, muoloke, amuna onse amphamvu ovala zida zao, pamaso pa abale anu ana a Israele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa