Masalimo 136:13 - Buku Lopatulika13 Amene anagawa magawo Nyanja Yofiira; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Amene anagawa magawo Nyanja Yofiira; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Adagaŵa pakati Nyanja Yofiira, pakuti chikondi chake nchamuyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Amene anagawa Nyanja Yofiira pakati, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. Onani mutuwo |