Masalimo 136:14 - Buku Lopatulika14 Napititsa Israele pakati pake; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Napititsa Israele pakati pake; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Adaolotsa Aisraele pakati pake, pakuti chikondi chake nchamuyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Nadutsitsa Israeli pakati pa nyanjayo, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. Onani mutuwo |