Masalimo 135:7 - Buku Lopatulika7 Akweza mitambo ichokere ku malekezero a dziko lapansi; ang'animitsa mphezi zidzetse mvula; atulutsa mphepo mosungira mwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Akweza mitambo ichokere ku malekezero a dziko lapansi; ang'animitsa mphezi zidzetse mvula; atulutsa mphepo mosungira mwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ndiye amene amatulutsa mitambo ku mathero a dziko lapansi, amene amachititsa zing'aning'ani za mvula, amene amaombetsa mphepo kuchokera m'nkhokwe zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iye amatulutsa mitambo kuchokera ku malekezero a dziko lapansi, amatumiza zingʼaningʼani pamodzi ndi mvula ndipo amatulutsa mphepo ku malo ake osungiramo. Onani mutuwo |