Masalimo 135:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti Yehova anadzisankhira Yakobo, Israele, akhale chuma chake chenicheni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti Yehova anadzisankhira Yakobo, Israele, akhale chuma chake chenicheni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Wadzisankhulira Yakobe kuti akhale wake, Israele kuti akhale chuma chake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pakuti Yehova wasankha Yakobo kuti akhale wake, Israeli kuti akhale chuma chake chapamtima. Onani mutuwo |