Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 135:3 - Buku Lopatulika

3 Lemekezani Yehova; pakuti Yehova ndiye wabwino; muimbire zolemekeza dzina lake; pakuti nkokondweretsa kutero.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Lemekezani Yehova; pakuti Yehova ndiye wabwino; muimbire zolemekeza dzina lake; pakuti nkokondweretsa kutero.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Tamandani Chauta, pakuti ngwabwino. Muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake, pakuti nlokoma kwambiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Tamandani Yehova, pakuti Yehova ndi wabwino; imbani nyimbo zotamanda dzina lake, pakuti nʼkokoma kutero,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 135:3
12 Mawu Ofanana  

Pakuti Yehova ndiye wabwino; chifundo chake chimanka muyaya; ndi chikhulupiriko chake ku mibadwomibadwo.


Aleluya. Yamikani Yehova; pakuti Iye ndiye wabwino: Pakuti chifundo chake nchosatha.


Yamikani Yehova pakuti Iye ndiye wabwino; pakuti chifundo chake nchosatha.


Yamikani Yehova; pakuti Iye ndiye wabwino; pakuti chifundo chake nchosatha.


Inu ndinu wabwino, ndi wakuchita zabwino; mundiphunzitse malemba anu.


Yamikani Yehova pakuti ndiye wabwino; pakuti chifundo chake nchosatha.


Aleluya; Pakuti kuimbira zomlemekeza Mulungu wathu nkokoma; pakuti chikondweretsa ichi, chilemekezo chiyenera.


Fuulani mokondwera mwa Yehova, inu olungama mtima, oongoka mtima ayenera kulemekeza.


Mudzakhutitsa moyo wanga ngati ndi mafuta ndi zonona; ndipo pakamwa panga ndidzakulemekezani ndi milomo yakufuula mokondwera.


Ndipo Iye anati kwa iye, Undifunsiranji za chinthu chabwino? Alipo Mmodzi ndiye wabwino: koma ngati ufuna kulowa m'moyo, sunga malamulo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa