Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 135:2 - Buku Lopatulika

2 Inu akuimirira m'nyumba ya Yehova, m'mabwalo a nyumba ya Mulungu wathu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Inu akuimirira m'nyumba ya Yehova, m'mabwalo a nyumba ya Mulungu wathu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 inu amene mumatumikira m'Nyumba ya Chauta, m'mabwalo a Nyumba ya Mulungu wathu!

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 amene mumatumikira mʼnyumba ya Yehova, mʼmabwalo a nyumba ya Mulungu wathu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 135:2
9 Mawu Ofanana  

ndi kuimirira m'mawa ndi m'mawa kuyamika ndi kulemekeza Yehova, momwemonso madzulo;


Ndipo muimirire m'malo opatulika, monga mwa magawidwe a nyumba za makolo za abale anu ana a anthu, akhale nalo onse gawo la nyumba ya makolo ya Alevi.


Nati Alevi, Yesuwa, ndi Kadimiyele, Bani, Hasabineya, Serebiya, Hodiya, Sebaniya, ndi Petahiya, Imirirani, lemekezani Yehova Mulungu wanu kunthawi za nthawi; ndipo lilemekezeke dzina lanu la ulemerero, lokuzika loposa chilemekezo ndi chiyamiko chonse.


M'mabwalo a nyumba ya Yehova, pakati pa inu, Yerusalemu. Aleluya.


Taonani, lemekezani Yehova, atumiki a Yehova inu nonse, akuimirira m'nyumba ya Yehova usiku.


Iwo ookedwa m'nyumba ya Yehova, adzaphuka m'mabwalo a Mulungu wathu.


Mpatseni Yehova ulemerero wa dzina lake; bwerani nacho chopereka, ndipo fikani kumabwalo ake.


zaka zisanu ndi ziwiri, ndipo anali wamasiye wa kufikira zaka zake makumi asanu ndi atatu mphambu zinai, amene sankachoka ku Kachisi, wotumikira Mulungu ndi kusala kudya ndi kupemphera usiku ndi usana.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa