Masalimo 135:20 - Buku Lopatulika20 A nyumba ya Levi inu, lemekezani Yehova: Inu akuopa Yehova, lemekezani Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 A nyumba ya Levi inu, lemekezani Yehova: Inu akuopa Yehova, lemekezani Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Inu a banja la Levi, tamandani Chauta! Inu amene mumaopa Chauta, tamandani Chauta! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Inu nyumba ya Levi, tamandani Yehova; Inu amene mumaopa Iye, tamandani Yehova. Onani mutuwo |