Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 135:19 - Buku Lopatulika

19 A nyumba ya Israele inu, lemekezani Yehova: A nyumba ya Aroni inu, lemekezani Yehova:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 A nyumba ya Israele inu, lemekezani Yehova: A nyumba ya Aroni inu, lemekezani Yehova:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Inu a m'banja la Israele, tamandani Chauta! Inu a m'banja la Aroni, tamandani Chauta!

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Inu nyumba ya Israeli, tamandani Yehova; inu nyumba ya Aaroni, tamandani Yehova;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 135:19
8 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide anati kwa khamu lonse, Mulemekeze tsono Yehova Mulungu wanu. Ndi khamu lonse linalemekeza Yehova Mulungu wa makolo ao, nawerama, nalambira Yehova, ndi mfumu.


Yehova watikumbukira; adzatidalitsa: adzadalitsa nyumba ya Israele; adzadalitsa nyumba ya Aroni.


Ntchito zanu zonse zidzakuyamikani, Yehova; ndi okondedwa anu adzakulemekezani.


Ndipo anakweza nyanga ya anthu ake, chilemekezo cha okondedwa ake onse; ndiwo ana a Israele, anthu a pafupi pa Iye. Aleluya.


Ndipo mau anachokera kumpando wachifumu, ndi kunena, Lemekezani Mulungu wathu akapolo ake onse akumuopa Iye, aang'ono ndi aakulu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa