Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 135:18 - Buku Lopatulika

18 Akuwapanga adzafanana nao; inde, onse akuwakhulupirira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Akuwapanga adzafanana nao; inde, onse akuwakhulupirira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Anthu amene amapanga mafanowo afanefane nawo, chimodzimodzi onse amene amaŵakhulupirira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Iwo amene amapanga mafanowo adzakhala ngati mafanowo, chimodzimodzinso iwo amene amadalira mafanowo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 135:18
6 Mawu Ofanana  

Adzafanana nao iwo akuwapanga; ndi onse akuwakhulupirira.


Onse akutumikira fano losema, akudzitamandira nao mafano, achite manyazi: Mgwadireni Iye, milungu yonse inu.


Iwo adzabwezedwa m'mbuyo, adzakhala ndi manyazi ambiri amene akhulupirira mafano osemedwa, nati kwa mafano oyengeka, Inu ndinu milungu yathu.


Koma onse pamodzi apulukira ndi kupusa; mtengo ndiwo chilangizo, chopanda pake.


mwa amene mulungu wa nthawi ino ya pansi pano anachititsa khungu maganizo ao a osakhulupirira, kuti chiwalitsiro cha Uthenga Wabwino wa ulemerero wa Khristu, amene ali chithunzithunzi cha Mulungu, chisawawalire.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa