Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 135:17 - Buku Lopatulika

17 makutu ali nao, koma osamva; inde, pakamwa pao palibe mpweya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 makutu ali nao, koma osamva; inde, pakamwa pao palibe mpweya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Makutu ali nawo, koma saamva, ndipo alibe mpweya m'kamwa mwao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 makutu ali nawo, koma sakumva ndipo mʼkamwa mwawo mulibe mpweya uliwonse.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 135:17
4 Mawu Ofanana  

polankhula Iye, pali unyinji wa madzi m'mwamba, ndipo akweretsa nkhungu ku malekezero a dziko lapansi, alenga mphezi idzetse mvula, natulutsa mphepo m'zosungira zake.


Anthu onse ali opulukira ndi opanda nzeru; wakusula golide achitidwa manyazi ndi fanizo lake losema; pakuti fanizo lake loyenga lili bodza, mulibe mpweya m'menemo.


Ndipo tsopano aonjeza kuchimwa, nadzipangira mafano oyenga a siliva wao, mafano monga mwa nzeru zao, onsewo ntchito ya amisiri; anena za iwo, Anthu ophera nsembe apsompsone anaang'ombe.


Tsoka iye wakunena kwa mtengo, Galamuka; ndi kwa mwala wosalankhula, Nyamuka! Kodi ichi chiphunzitsa? Taona chakutidwa ndi golide ndi siliva, ndi m'kati mwake mulibe mpweya konse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa