Masalimo 135:16 - Buku Lopatulika16 Pakamwa ali napo koma osalankhula; maso ali nao, koma osapenya; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Pakamwa ali napo koma osalankhula; maso ali nao, koma osapenya; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Pakamwa ali napo, koma salankhula, maso ali nawo, koma sapenya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Pakamwa ali napo koma sayankhula maso ali nawo, koma sapenya; Onani mutuwo |