Masalimo 135:15 - Buku Lopatulika15 Mafano a amitundu ndiwo siliva ndi golide, ntchito ya manja a anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Mafano a amitundu ndiwo siliva ndi golide, ntchito ya manja a anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Mafano a mitundu ina ya anthu ndi asiliva ndi agolide chabe, ndi opangidwa ndi manja a anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Mafano a mitundu ya anthu ndi siliva ndi golide, opangidwa ndi manja a anthu. Onani mutuwo |