Masalimo 132:10 - Buku Lopatulika10 Chifukwa cha Davide mtumiki wanu musabweze nkhope ya wodzozedwa wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Chifukwa cha Davide mtumiki wanu musabweze nkhope ya wodzozedwa wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Chifukwa cha zimene mudalonjeza kwa mtumiki wanu Davide, musakane nkhope ya wodzozedwa wanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Chifukwa cha Davide mtumiki wanu, musakane wodzozedwa wanu. Onani mutuwo |