Masalimo 132:1 - Buku Lopatulika1 Yehova, kumbukirani Davide kuzunzika kwake konse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Yehova, kumbukirani Davide kuzunzika kwake konse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Inu Chauta, mukumbukire Davide ndi mavuto onse amene adaŵapirira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Inu Yehova, kumbukirani Davide ndi mavuto onse anapirira. Onani mutuwo |