Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 131:3 - Buku Lopatulika

3 Israele, uyembekezere Yehova, kuyambira tsopano kufikira kosatha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Israele, uyembekezere Yehova, kuyambira tsopano kufikira kosatha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Iwe Israele, khulupirira Chauta kuyambira tsopano mpaka muyaya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Yembekeza Yehova, iwe Israeli, kuyambira tsopano mpaka muyaya.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 131:3
7 Mawu Ofanana  

Koma ife tidzalemekeza Yehova kuyambira tsopano kufikira nthawi yonse. Aleluya.


Yehova adzasungira kutuluka kwako ndi kulowa kwako, kuyambira tsopano kufikira nthawi zonse.


Israele, uyembekezere Yehova; chifukwa kwa Yehova kuli chifundo, kwaonso kuchulukira chiombolo.


Wodala munthu amene akhala naye Mulungu wa Yakobo kuti amthandize, chiyembekezo chake chili pa Yehova, Mulungu wake.


Khulupirirani Yehova nthawi zamuyaya, pakuti mwa Ambuye Yehova muli thanthwe lachikhalire.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa