Masalimo 13:4 - Buku Lopatulika4 kuti anganene mdani wanga, Ndamgonjetsa; ndipo angakondwere otsutsana nane posunthika ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 kuti anganene mdani wanga, Ndamlaka; ndipo angakondwere otsutsana nane posunthika ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mdani wanga asati, “Ndampambana,” adani anga onse asakondwere poona kuti ndagwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 mdani wanga adzati, “Ndamugonjetsa,” ndipo adani anga adzakondwera pamene ine ndagwa. Onani mutuwo |