Masalimo 13:3 - Buku Lopatulika3 Penyani, ndiyankheni, Yehova Mulungu wanga. Penyetsani maso anga, kuti ndingagone tulo ta imfa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Penyani, ndiyankheni, Yehova Mulungu wanga. Penyetsani maso anga, kuti ndingagone tulo ta imfa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mundikumbukire ndipo mundiyankhe, Inu Chauta, Mulungu wanga. Mundiwunikire kuti ndingagone tulo tofa nato. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndiyangʼaneni ndi kundiyankha, Inu Yehova Mulungu wanga. Walitsani maso anga kuti ndingafe; Onani mutuwo |