Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 129:3 - Buku Lopatulika

3 Olima analima pamsana panga; anatalikitsa mipere yao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Olima analima pamsana panga; anatalikitsa mipere yao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 “Pondikwapula adani anga adachita ngati kulima pamsana panga, kulima mizere yaitali.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Anthu otipula analima pa msana panga ndipo anapangapo mizere yayitali:

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 129:3
4 Mawu Ofanana  

Kodi ukhoza kumanga njati ndi lamba lake ilime m'mchera? Kapena idzakutsata kodi kufafaniza nthumbira m'zigwa?


Mafupa athu amwazika pakamwa pa manda, monga ngati akumba nanyimphula nthaka yapansi.


Ndinapereka msana wanga kwa omenya, ndi masaya anga kwa iwo amene anakudzula tsitsi langa; sindinabisire nkhope yanga manyazi ndi kulavulidwa.


Ndidzachiika m'dzanja la iwo amene avutitsa iwe; amene anena kumoyo wako, Gwada pansi kuti ife tipite; ndipo iwe wagonetsa pamsana pako monga pansi, ndi monga khwalala kwa iwo amene apita pamenepo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa