Masalimo 128:2 - Buku Lopatulika2 Pakuti udzadya za ntchito ya manja ako; wodala iwe, ndipo kudzakukomera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pakuti udzadya za ntchito ya manja ako; wodala iwe, ndipo kudzakukomera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Udzadya zimene manja ako adagwirira ntchito. Udzasangalala, ndipo zinthu zidzakuyendera bwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Udzadya chipatso cha ntchito yako; madalitso ndi chuma zidzakhala zako. Onani mutuwo |