Masalimo 127:1 - Buku Lopatulika1 Akapanda kumanga nyumba Yehova, akuimanga agwiritsa ntchito chabe; akapanda kusunga mzinda Yehova, mlonda adikira chabe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Akapanda kumanga nyumba Yehova, akuimanga agwiritsa ntchito chabe; akapanda kusunga mudzi Yehova, mlonda adikira chabe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Chauta akapanda kumanga nawo nyumba, omanga nyumbayo angogwira ntchito pachabe. Chauta akapanda kulonda nawo mzinda, mlonda angochezera pachabe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yehova akapanda kumanga nyumba, omanga nyumbayo agwira ntchito pachabe. Yehova akapanda kulondera mzinda, mlonda akanangolondera pachabe. Onani mutuwo |