Masalimo 123:4 - Buku Lopatulika4 Moyo wathu wakhuta ndithu ndi kuseka kwa iwo osasowa kanthu, ndi mnyozo wa odzikuza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Moyo wathu wakhuta ndithu ndi kuseka kwa iwo osasowa kanthu, ndi mnyozo wa odzikuza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Pa nthaŵi yaitali, anthu olemera akhala akutinyodola, anthu onyada akhala akutinyoza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ife tapirira mnyozo wambiri kuchokera kwa anthu odzikuza, chitonzo chachikulu kuchokera kwa anthu onyada. Onani mutuwo |