Masalimo 123:3 - Buku Lopatulika3 Mutichitire chifundo, Yehova, mutichitire chifundo; pakuti takhuta kwambiri ndi mnyozo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Mutichitire chifundo, Yehova, mutichitire chifundo; pakuti takhuta kwambiri ndi mnyozo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mutichitire chifundo, Inu Chauta, mutichitire chifundo, pakuti adani athu atinyoza kopitirira malire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mutichitire chifundo, Inu Yehova mutichitire chifundo, pakuti tapirira chitonzo chachikulu. Onani mutuwo |