Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 122:9 - Buku Lopatulika

9 Chifukwa cha nyumba ya Yehova Mulungu wathu ndidzakufunira zokoma.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Chifukwa cha nyumba ya Yehova Mulungu wathu ndidzakufunira zokoma.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Chifukwa cha Nyumba ya Chauta, Mulungu wathu, ndidzakupemphera zabwino.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Chifukwa cha Nyumba ya Yehova Mulungu wathu, ndidzakufunira zabwino.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 122:9
11 Mawu Ofanana  

Ndiponso popeza ndikondwera nayo nyumba ya Mulungu wanga, chuma changachanga cha golide ndi siliva ndili nacho ndichipereka kunyumba ya Mulungu wanga, moonjezera ndi zonse ndazikonzeratu nyumba yopatulikayo;


Mundikumbukire Mulungu wanga mwa ichi, nimusafafanize zokoma zanga ndinazichitira nyumba ya Mulungu wanga, ndi maudikiro ake.


Atamva Sanibalati Muhoroni, ndi Tobiya kapoloyo Mwamoni, chidawaipira kwakukulu, kuti wadza munthu kuwafunira ana a Israele chokoma.


Pakuti Mordekai Myuda anatsatana naye mfumu Ahasuwero, nakhala wamkulu mwa Ayuda, navomerezeka mwa unyinji wa abale ake wakufunira a mtundu wake zokoma, ndi wakunena za mtendere kwa mbeu yake yonse.


Yehova, ndikonda chikhalidwe cha nyumba yanu, ndi malo akukhalamo ulemerero wanu.


Pakuti changu cha pa nyumba yanu chandidya; ndi zotonza za iwo otonza Inu zandigwera ine.


Pakuti tsiku limodzi m'mabwalo anu likoma koposa masiku ambirimbiri akukhala pena. Kukhala ine wapakhomo m'nyumba ya Mulungu wanga, kundikonda ine koposa kugonera m'mahema a choipa.


Ophunzira ake anakumbukira kuti kunalembedwa, Changu cha pa nyumba yanu chandidya ine.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa