Masalimo 122:8 - Buku Lopatulika8 Chifukwa cha abale anga ndi mabwenzi anga, ndidzanena tsopano, Mukhale mtendere mwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Chifukwa cha abale anga ndi mabwenzi anga, ndidzanena tsopano, Mukhale mtendere mwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Chifukwa cha abale anga ndi abwenzi anga ndidzanena kuti, “Mtendere ukhaledi m'kati mwako.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Chifukwa cha abale anga ndi abwenzi anga ndidzati, “Mtendere ukhale mʼkati mwako.” Onani mutuwo |