Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 122:7 - Buku Lopatulika

7 M'linga mwako mukhale mtendere, m'nyumba za mafumu mukhale phindu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 M'linga mwako mukhale mtendere, m'nyumba za mafumu mukhale phindu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Mtendere ukhale m'kati mwa makoma ako, bata likhale m'nyumba zako zachifumu.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Mukhale mtendere mʼkati mwa makoma ako, ndipo mʼnyumba zako zaufumu mukhale chitetezo.”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 122:7
7 Mawu Ofanana  

Pamenepo mzimu unavala Amasai, ndiye wamkulu wa makumi atatuwo, nati iye, Ndife anu, Davide, tivomerezana nanu mwana wa Yese inu: mtendere, mtendere ukhale ndi inu, ndi mtendere ukhale ndi athandizi anu; pakuti Mulungu wanu akuthandizani. Ndipo Davide anawalandira, nawaika akulu a magulu.


Penyetsetsani malinga ake, yesetsani zinyumba zake; kuti mukaziwerengere mibadwo ikudza m'mbuyo.


Mulungu adziwika m'zinyumba zake ngati msanje.


Ndipo ana ako onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova; ndipo mtendere wa ana ako udzakhala waukulu.


Za kuwonjezera ulamuliro wake, ndi za mtendere sizidzatha pa mpando wachifumu wa Davide, ndi pa ufumu wake, kuukhazikitsa, ndi kuuchirikiza ndi chiweruziro ndi chilungamo kuyambira tsopano ndi kunkabe nthawi zonse. Changu cha Yehova wa makamu chidzachita zimenezi.


Mtendere ndikusiyirani inu, mtendere wanga ndikupatsani; Ine sindikupatsani inu monga dziko lapansi lipatsa. Mtima wanu usavutike, kapena usachite mantha.


Ndipo chipatso cha chilungamo chifesedwa mumtendere kwa iwo akuchita mtendere.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa