Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 122:5 - Buku Lopatulika

5 Pakuti pamenepo anaika mipando ya chiweruzo, mipando ya nyumba ya Davide.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Pakuti pamenepo anaika mipando ya chiweruzo, mipando ya nyumba ya Davide.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Kumeneko adaikako mipando yaufumu yoweruzira, mipando yake ya banja la Davide.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Kumeneko anayikako mipando yaufumu yachiweruzo, mipando yaufumu ya nyumba ya Davide.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 122:5
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Benaya mwana wa Yehoyada anayang'anira Akereti ndi Apeleti. Ndipo ana a Davide anali ansembe ake.


Ndipo anamanga khonde la mpando wachifumu loweruziramo iye, ndilo khonde la milandu, ndipo linayalidwa ndi mkungudza pansi ndi posanja.


Ndipo Rehobowamu anaika Abiya mwana wa Maaka akhale wamkulu, kalonga mwa abale ake; ndiko kuti adzamlonga ufumu.


Yehosafati anaikanso mu Yerusalemu Alevi, ndi ansembe ena, ndi akulu a nyumba za makolo mu Israele, aweruzire Yehova, nanena milandu. Ndipo anabwerera kudza ku Yerusalemu.


Ndipo kudzali, pakukhala iye pa mpando wachifumu wa ufumu wake, adzilemberere chofanana cha chilamulo ichi m'buku, achitenge pa ichi chili pamaso pa ansembe Alevi;


Ukakukanikani mlandu pouweruza, ndiwo wakunena zamwazi, kapena zakutsutsana, kapena zakupandana, ndiyo milandu yakutengana m'midzi mwanu; pamenepo muziuka ndi kukwera kunka ku malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankha;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa