Masalimo 121:5 - Buku Lopatulika5 Yehova ndiye wakukusunga; Yehova ndiye mthunzi wako wa kudzanja lako lamanja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Yehova ndiye wakukusunga; Yehova ndiye mthunzi wako wa kudzanja lako lamanja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Chauta ndiye amene amakusunga, Chauta ndiye mtetezi wako ali ku dzanja lako lamanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Yehova ndiye amene amakusunga; Yehova ndiye mthunzi wako ku dzanja lako lamanja. Onani mutuwo |