Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 121:4 - Buku Lopatulika

4 Taonani, wakusunga Israele sadzaodzera kapena kugona.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Taonani, wakusunga Israele sadzaodzera kapena kugona.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Zoonadi, amene amasunga Israele, ndithu sadzaodzera kapena kugona.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Taonani, Iye amene amasunga Israeli sadzawodzera kapena kugona.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 121:4
7 Mawu Ofanana  

Ndipo pausana Eliya anawaseka, nati, Kwezani mau, popeza ndiye mulungu; kapena alikulingirira, kapena wapambuka, kapena ali paulendo, kaya agona, adzagalamuka.


Akapanda kumanga nyumba Yehova, akuimanga agwiritsa ntchito chabe; akapanda kusunga mzinda Yehova, mlonda adikira chabe.


Yehova ndiye kuunika kwanga ndi chipulumutso changa; ndidzaopa yani? Yehova ndiye mphamvu ya moyo wanga; ndidzachita mantha ndi yani?


Pompo ndinapereka mtima wanga kudziwa nzeru, ndi kupenya ntchito zichitidwa pansi pano; kuti anthu saona tulo konse ndi maso ao ngakhale usana ngakhale usiku;


Ine Yehova ndiusunga uwo; ndidzauthirira madzi nthawi zonse; ndidzausunga usiku ndi usana, kuti angauipse.


Chifukwa chake ali kumpando wachifumu wa Mulungu; ndipo amtumikira Iye usana ndi usiku mu Kachisi mwake; ndipo Iye wakukhala pa mpando wachifumu adzawachitira mthunzi,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa