Masalimo 121:3 - Buku Lopatulika3 Sadzalola phazi lako literereke: Iye amene akusunga sadzaodzera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Sadzalola phazi lako literereke: Iye amene akusunga sadzaodzera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Sadzalola phazi lako kuti literereke, Iye amene amakusunga sadzaodzera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Sadzalola kuti phazi lako literereke; Iye amene amakusunga sadzawodzera. Onani mutuwo |