Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 121:2 - Buku Lopatulika

2 Thandizo langa lidzera kwa Yehova, wakulenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Thandizo langa lidzera kwa Yehova, wakulenga zakumwamba ndi dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Chithandizo changa nchochokera kwa Chauta, amene adalenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Thandizo langa limachokera kwa Yehova, wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 121:2
10 Mawu Ofanana  

Pachiyambi Mulungu adalenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Odalitsika inu a kwa Yehova, wakulenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Thandizo lathu lili m'dzina la Yehova, wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Mulungu ndiye pothawirapo pathu ndi mphamvu yathu, thandizo lopezekeratu m'masautso.


Pakuti Ine Yehova Mulungu wako ndidzagwira dzanja lako lamanja, ndi kunena kwa iwe, Usaope ndidzakuthandiza iwe.


Koma Yehova ali ndi ine ngati wamphamvu ndi woopsa; chifukwa chake ondisautsa adzaphunthwa, sadzandilala; adzakhala ndi manyazi ambiri, chifukwa sanachite chanzeru, ngakhale ndi kunyazitsa kwamuyaya kumene sikudzaiwalika.


Israele, chikuononga ndi ichi, chakuti utsutsana ndi Ine, chithandizo chako.


Kotero kuti tinena molimbika mtima, Mthandizi wanga ndiye Ambuye; sindidzaopa; adzandichitira chiyani munthu?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa