Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 121:1 - Buku Lopatulika

1 Ndikweza maso anga kumapiri: Thandizo langa lidzera kuti?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndikweza maso anga kumapiri: Thandizo langa lidzera kuti?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Ndimakweza maso anga ku mapiri. Kodi chithandizo changa chimachokera kuti?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Ndikweza maso anga ku mapiri; kodi thandizo langa limachokera kuti?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 121:1
8 Mawu Ofanana  

Ndinafuulira kwa Yehova mu msauko wanga, ndipo anandivomereza.


Ndikweza maso anga kwa Inu, kwa Inu wakukhala kumwamba.


Koma Ine ndadzoza mfumu yanga Pa Ziyoni, phiri langa loyera.


koma anasankha fuko la Yuda, Phiri la Ziyoni limene analikonda.


Maziko ake ali m'mapiri oyera.


Ndipo anthu ambiri adzanka, nati, Tiyeni tikwere kunka kuphiri la Yehova, kunyumba ya Mulungu wa Yakobo; ndipo Iye adzatiphunzitsa za njira zake, ndipo tidzayenda m'mayendedwe ake; chifukwa mu Ziyoni mudzatuluka chilamulo, ndi mau a Yehova kuchokera mu Yerusalemu.


Ndithu akhulupirira mwachabe chithandizo cha kuzitunda, ndi phokoso la kumapiri; ndithu mwa Yehova Mulungu wathu muli chipulumutso cha Israele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa