Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 120:7 - Buku Lopatulika

7 Ine ndikuti, Mtendere; koma polankhula ine, iwowa akuti, Nkhondo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ine ndikuti, Mtendere; koma polankhula ine, iwowa akuti, Nkhondo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Ine ndimafuna mtendere, koma ndikalankhula za mtendere, iwo amafuna nkhondo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ine ndine munthu wamtendere; koma ndikamayankhula, iwo amafuna nkhondo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 120:7
12 Mawu Ofanana  

Ine ndine wa awo amene ali amtendere ndi okhulupirika mu Israele; inu mulikufuna kuononga mzinda ndi mai wa mu Israele; mudzamezeranji cholowa cha Yehova?


M'malo mwa chikondi changa andibwezera udani; koma ine, kupemphera ndiko.


Futuka pazoipa, nuchite zabwino, funa mtendere ndi kuulondola.


Pakuti salankhula zamtendere, koma apangira chiwembu odekha m'dziko.


Anatulutsa manja ake awagwire iwo akuyanjana naye, anaipsa pangano lake.


Odala ali akuchita mtendere; chifukwa adzatchedwa ana a Mulungu.


Ngati nkutheka, monga momwe mukhoza, khalani ndi mtendere ndi anthu onse.


Londolani mtendere ndi anthu onse, ndi chiyeretso chimene, akapanda ichi, palibe mmodzi adzaona Ambuye:


Ndipo Yefita anatumanso mithenga kwa mfumu ya ana a Amoni;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa