Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 120:6 - Buku Lopatulika

6 Moyo wanga unakhalitsa nthawi pamodzi ndi iye wakudana nao mtendere.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Moyo wanga unakhalitsa nthawi pamodzi ndi iye wakudana nao mtendere.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Ndakhala nthaŵi yaitali pakati pa anthu odana ndi mtendere.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Kwa nthawi yayitali ndakhala pakati pa iwo amene amadana ndi mtendere.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 120:6
6 Mawu Ofanana  

Moyo wanga uli pakati pa mikango; ndigona pakati pa oyaka moto, ndiwo ana a anthu amene mano ao ali nthungo ndi mivi, ndipo lilime lao ndilo lupanga lakuthwa.


Ndipo iwe, wobadwa ndi munthu iwe, usawaopa, kapena kuopa mau ao; ingakhale mitungwi ndi minga ikhala ndi iwe, nukhala pakati pa zinkhanira, usaopa mau ao kapena kuopsedwa ndi nkhope zao; pakuti ndiwo nyumba yopanduka.


Taonani, Ine ndikutumizani inu monga nkhosa pakati pa mimbulu; chifukwa chake khalani ochenjera monga njoka, ndi oona mtima monga nkhunda.


ndipo apabanja ake a munthu adzakhala adani ake.


Pakuti kale ifenso tinali opusa, osamvera, onyengeka, akuchitira ukapolo zilakolako ndi zokondweretsa za mitundumitundu, okhala m'dumbo ndi njiru, odanidwa, odana wina ndi mnzake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa