Masalimo 121:6 - Buku Lopatulika6 Dzuwa silidzawamba usana, mwezi sudzakupanda usiku. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Dzuwa silidzawamba usana, mwezi sudzakupanda usiku. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Dzuŵa silidzakupweteka masana, mwezi sudzakuvuta usiku. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Dzuwa silidzakupweteka nthawi ya masana, kapena mwezi nthawi ya usiku. Onani mutuwo |