Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 120:3 - Buku Lopatulika

3 Adzakuninkhanji, adzakuonjezeranji, lilime lonyenga iwe?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Adzakuninkhanji, adzakuonjezeranji, lilime lonyenga iwe?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Mulungu adzakuchitani chiyani, anthu onyenganu? Kodi adzakupatsani chilango cha mtundu wanji?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Kodi adzakuchitani chiyani, ndipo adzawonjezerapo zotani, inu anthu achinyengo?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 120:3
3 Mawu Ofanana  

Pakuti chiyembekezo cha wonyoza Mulungu nchiyani pomlikhatu Mulungu, pomchotsera moyo wake?


Pakuti munthu adzapindulanji, akalandira dziko lonse, nataya moyo wake? Kapena munthu adzaperekanji chosintha ndi moyo wake?


Ndipo munali nazo zobala zanji nthawi ija, m'zinthu zimene muchita nazo manyazi tsopano? Pakuti chimaliziro cha zinthu izi chili imfa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa