Masalimo 120:2 - Buku Lopatulika2 Yehova, landitsani moyo wanga kumilomo ya mabodza, ndi kulilime lonyenga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Yehova, landitsani moyo wanga kumilomo ya mabodza, ndi kulilime lonyenga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ndimati, “Pulumutseni, Inu Chauta, kwa anthu onama ndi kwa anthu onyenga.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Pulumutseni Yehova ku milomo yabodza, ndi kwa anthu achinyengo. Onani mutuwo |