Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 12:8 - Buku Lopatulika

8 Oipa amayenda mozungulirazungulira, potamanda iwo chonyansa mwa ana a anthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Oipa amayenda mozungulirazungulira, potamanda iwo chonyansa mwa ana a anthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 pakuti anthu oipa amangoyendayenda ponseponse, ndipo anzao amayamikira zochita zao zoipa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Oyipa amangoyendayenda ponseponse anthu akamayamikira zochita zawo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 12:8
11 Mawu Ofanana  

Ndiwo ana a opusa, inde ana a anthu opanda dzina; anawaingitsa kuwachotsa m'dziko.


Mkulu akamvera chinyengo, atumiki ake onse ali oipa.


Ndi m'malo mwake adzauka munthu woluluka, amene anthu sanampatse ulemu wa ufumu, koma adzafika kachetechete, nadzalanda ufumu ndi mau osyasyalika.


Efuremu azunzika, apsinjika pa mlanduwo; pakuti anafuna mwini wake kutsata lamulolo.


Pakuti asunga malemba a Omuri, ndi ntchito za nyumba ya Ahabu, ndipo mumayenda mu uphungu wao; kuti ndikusandulize bwinja, ndi okhalamo chotsonya; ndipo mudzasenza chitonzo cha anthu anga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa