Masalimo 12:1 - Buku Lopatulika1 Pulumutsani, Yehova; pakuti wofatsa wasowa; pakuti okhulupirika achepa mwa ana a anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pulumutsani, Yehova; pakuti wofatsa wasowa; pakuti okhulupirika achepa mwa ana a anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Thandizeni, Inu Chauta, palibenso munthu wosamala za Inu, okhulupirika sapezekanso pakati pa anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Thandizeni Yehova pakuti palibe munthu wokhulupirika; okhulupirika akusowa pakati pa anthu. Onani mutuwo |